NEEF Ichita mkumano ndi adindo ku Mangochi

Bungwe la NEEF lachita mkumano ndi adindo am’boma la Mangochi umene ukuchitikira pa Hall ya Khonsolo ya Bomali. Cholinga cham’kumanowu malinga ndi mkulu wa Bungwe la NEEF a Humphrey Mdyetseni, ndikufuna kufotokozera adindowa momwe NEEF ikugwilira ntchito m’bomali komanso kuwapempha kuti athandize bungweli kuti lizikwanitsa kutolera ngongole zonse zomwe lapereka m’boma la Mangochi. Malinga ndi…

Read More